Mateyu 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Musachite mantha ndi amene amapha thupi koma sangathe kupha moyo.+ Mʼmalomwake, muziopa amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe mʼGehena.*+ Mateyu 26:75 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 75 Ndiyeno Petulo anakumbukira mawu a Yesu aja akuti: “Tambala asanalire, udzandikana katatu.”+ Ndipo anatuluka panja nʼkuyamba kulira mopwetekedwa mtima kwambiri.
28 Musachite mantha ndi amene amapha thupi koma sangathe kupha moyo.+ Mʼmalomwake, muziopa amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe mʼGehena.*+
75 Ndiyeno Petulo anakumbukira mawu a Yesu aja akuti: “Tambala asanalire, udzandikana katatu.”+ Ndipo anatuluka panja nʼkuyamba kulira mopwetekedwa mtima kwambiri.