Levitiko 20:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Munthu akatemberera* bambo kapena mayi ake, aziphedwa ndithu.+ Mlandu wa magazi ake ukhale pa iye chifukwa watemberera bambo ake kapena mayi ake. Deuteronomo 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ngati munthu ali ndi mwana wamwamuna wosamvera komanso wopanduka, amene samvera bambo ake kapena mayi ake,+ ndipo ayesetsa kumulangiza koma amakana kuwamvera,+ Deuteronomo 21:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako amuna onse a mumzinda wawo azimuponya miyala nʼkumupha. Choncho muzichotsa woipayo pakati panu, ndipo Aisiraeli onse adzamva nʼkuchita mantha.+ Miyambo 20:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Aliyense amene amatemberera bambo ake komanso mayi ake,Nyale yake idzazimitsidwa kukagwa mdima.+
9 Munthu akatemberera* bambo kapena mayi ake, aziphedwa ndithu.+ Mlandu wa magazi ake ukhale pa iye chifukwa watemberera bambo ake kapena mayi ake.
18 Ngati munthu ali ndi mwana wamwamuna wosamvera komanso wopanduka, amene samvera bambo ake kapena mayi ake,+ ndipo ayesetsa kumulangiza koma amakana kuwamvera,+
21 Kenako amuna onse a mumzinda wawo azimuponya miyala nʼkumupha. Choncho muzichotsa woipayo pakati panu, ndipo Aisiraeli onse adzamva nʼkuchita mantha.+