1 Mafumu 4:29, 30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mulungu anapatsa Solomo nzeru, luso lozindikira komanso mtima womvetsa zinthu zambirimbiri ngati mchenga wa mʼmbali mwa nyanja.+ 30 Nzeru za Solomo zinaposa nzeru za anthu onse a Kumʼmawa komanso nzeru zonse za ku Iguputo.+
29 Mulungu anapatsa Solomo nzeru, luso lozindikira komanso mtima womvetsa zinthu zambirimbiri ngati mchenga wa mʼmbali mwa nyanja.+ 30 Nzeru za Solomo zinaposa nzeru za anthu onse a Kumʼmawa komanso nzeru zonse za ku Iguputo.+