Salimo 49:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chifukwa akadzamwalira sadzatenga china chilichonse.+Ulemerero wake sadzapita nawo limodzi.+ Luka 12:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma Mulungu anamuuza kuti, ‘Wopanda nzeru iwe, usiku womwe uno moyo wako aufuna. Nanga zinthu zimene wasungazi zidzakhala za ndani?’+ 1 Timoteyo 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pajatu sitinabwere ndi kanthu mʼdziko ndipo sitingachokemo ndi kanthu.+
20 Koma Mulungu anamuuza kuti, ‘Wopanda nzeru iwe, usiku womwe uno moyo wako aufuna. Nanga zinthu zimene wasungazi zidzakhala za ndani?’+