-
Yesaya 56:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 “Mʼnyumba mwanga ndiponso mkati mwa mpanda wanga ndidzawapatsa chipilala chachikumbutso ndiponso dzina,
Zomwe ndi zabwino kwambiri kuposa ana aamuna ndi aakazi.
Ndidzawapatsa dzina limene lidzakhalapo mpaka kalekale,
Dzina limene silidzatha.
-