Miyambo 16:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Munthu wosakwiya msanga+ ndi wabwino kuposa munthu wamphamvu,Ndipo munthu amene amalamulira mkwiyo wake amaposa munthu amene wagonjetsa mzinda.+ Yakobo 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Abale anga okondedwa, dziwani izi: Munthu aliyense azikhala wokonzeka kumvetsera, aziganiza kaye asanalankhule+ komanso asamafulumire kukwiya,+
32 Munthu wosakwiya msanga+ ndi wabwino kuposa munthu wamphamvu,Ndipo munthu amene amalamulira mkwiyo wake amaposa munthu amene wagonjetsa mzinda.+
19 Abale anga okondedwa, dziwani izi: Munthu aliyense azikhala wokonzeka kumvetsera, aziganiza kaye asanalankhule+ komanso asamafulumire kukwiya,+