-
Salimo 36:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Inu Yehova, mumapulumutsa munthu ndiponso nyama.+
-
-
Aroma 11:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Ndithudi, madalitso amene Mulungu amapereka ndi ochuluka kwambiri. Nzeru zake nʼzozama, ndiponso iye ndi wodziwa zinthu kwambiri. Ziweruzo zake ndi zovuta kuzimvetsa, ndipo ndani angatulukire njira zake?
-