15 Muzichitira Yehova Mulungu wanu chikondwerero chimenecho kwa masiku 7+ pamalo amene Yehova adzasankhe. Muzichita chikondwererochi chifukwa Yehova Mulungu wanu adzadalitsa zokolola zanu zonse ndi chilichonse chimene dzanja lanu likuchita,+ ndipo inu mudzakhala osangalala kwambiri.+