Miyambo 21:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Zinthu zimene munthu waulesi amalakalaka zidzamupha,Chifukwa manja ake amakana kugwira ntchito.+ Miyambo 24:33, 34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ukapitiriza kugona pangʼono, ukapitiriza katulo pangʼono,Ukapitiriza kupinda manja pangʼono kuti upume,34 Umphawi wako udzabwera ngati wachifwamba,Ndipo kusauka kwako kudzabwera ngati munthu wokhala ndi zida.+
33 Ukapitiriza kugona pangʼono, ukapitiriza katulo pangʼono,Ukapitiriza kupinda manja pangʼono kuti upume,34 Umphawi wako udzabwera ngati wachifwamba,Ndipo kusauka kwako kudzabwera ngati munthu wokhala ndi zida.+