1 Mafumu 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndikupatsanso zomwe sunapemphe.+ Ndikupatsa chuma ndi ulemerero,+ moti sikudzakhalanso mfumu ngati iwe pa nthawi yonse ya moyo wako.+ 1 Mafumu 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho Mfumu Solomo anali wolemera kwambiri+ ndiponso wanzeru+ kuposa mafumu ena onse a padziko lapansi.
13 Ndikupatsanso zomwe sunapemphe.+ Ndikupatsa chuma ndi ulemerero,+ moti sikudzakhalanso mfumu ngati iwe pa nthawi yonse ya moyo wako.+
23 Choncho Mfumu Solomo anali wolemera kwambiri+ ndiponso wanzeru+ kuposa mafumu ena onse a padziko lapansi.