-
Genesis 31:40, 41Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
40 Ndinkangokhalira kupsa ndi dzuwa masana komanso kuzizidwa ndi mphepo usiku, ndipo tulo sindinkationa.+ 41 Ndakhala mʼnyumba mwanu zaka 20. Ndakugwirirani ntchito zaka 14 kuti mundipatse ana anu aakazi awiriwa. Ndinagwiranso ntchito zaka zina 6 kuti mundipatse ziwetozi. Koma inu munkangosintha malipiro anga mpaka maulendo 10.+
-