Genesis 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Yehova Mulungu anati: “Si bwino kuti munthu azikhala yekha. Ndimupangira womuthandiza, monga mnzake womuyenerera.”+ Miyambo 27:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chitsulo chimanola chitsulo chinzake.Chimodzimodzinso munthu amanola munthu mnzake.*+
18 Kenako Yehova Mulungu anati: “Si bwino kuti munthu azikhala yekha. Ndimupangira womuthandiza, monga mnzake womuyenerera.”+