Miyambo 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mawu akachuluka sipalephera kukhala zolakwika,+Koma amene amalamulira milomo yake amachita zinthu mwanzeru.+ Miyambo 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Lilime la anthu anzeru limalankhula zabwino zimene anthuwo akudziwa,+Koma pakamwa pa zitsiru pamangolankhula mawu opusa.
19 Mawu akachuluka sipalephera kukhala zolakwika,+Koma amene amalamulira milomo yake amachita zinthu mwanzeru.+
2 Lilime la anthu anzeru limalankhula zabwino zimene anthuwo akudziwa,+Koma pakamwa pa zitsiru pamangolankhula mawu opusa.