Nyimbo ya Solomo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Wachikondi wanga ali ngati insa komanso mphoyo yaingʼono.+ Taonani! Iye waima kuseri kwa khoma la nyumba yathu.Akuyangʼana mʼmawindo,Akusuzumira pazotchingira mʼmawindo. Nyimbo ya Solomo 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mpaka kunja kutayamba kuwomba kamphepo kayaziyazi ndiponso mpaka mithunzi itachoka,Bwerera mwamsanga iwe wachikondi wanga,Kwera mapiri amene akutilekanitsa,* ngati insa+ komanso ngati mphoyo yaingʼono.”+
9 Wachikondi wanga ali ngati insa komanso mphoyo yaingʼono.+ Taonani! Iye waima kuseri kwa khoma la nyumba yathu.Akuyangʼana mʼmawindo,Akusuzumira pazotchingira mʼmawindo.
17 Mpaka kunja kutayamba kuwomba kamphepo kayaziyazi ndiponso mpaka mithunzi itachoka,Bwerera mwamsanga iwe wachikondi wanga,Kwera mapiri amene akutilekanitsa,* ngati insa+ komanso ngati mphoyo yaingʼono.”+