Nyimbo ya Solomo 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Ine ndinapita kumunda wa mitengo ya zipatso zokhala ndi mtedza,+Kuti ndikaone ngati yaphuka masamba atsopano mʼchigwa,*Kuti ndikaone ngati mitengo ya mpesa yaphukira,Ndiponso ngati mitengo ya makangaza yachita maluwa.
11 “Ine ndinapita kumunda wa mitengo ya zipatso zokhala ndi mtedza,+Kuti ndikaone ngati yaphuka masamba atsopano mʼchigwa,*Kuti ndikaone ngati mitengo ya mpesa yaphukira,Ndiponso ngati mitengo ya makangaza yachita maluwa.