Salimo 103:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye amakupatsa zinthu zabwino+ nthawi yonse ya moyo wako, zimene umakhutira nazo,Kuti ukhalebe wachinyamata ndi wamphamvu ngati chiwombankhanga.+
5 Iye amakupatsa zinthu zabwino+ nthawi yonse ya moyo wako, zimene umakhutira nazo,Kuti ukhalebe wachinyamata ndi wamphamvu ngati chiwombankhanga.+