Deuteronomo 33:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mulungu ndi malo ako othawirapo kuyambira kalekale,+Iye wakunyamula mʼmanja ake omwe adzakhalapo mpaka kalekale.+ Adzathamangitsa mdani pamaso pako,+Ndipo adzanena kuti, ‘Awonongeni!’+ Salimo 115:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aisiraeli inu, khulupirirani Yehova,+Iye ndi amene amakuthandizani komanso ndi chishango chanu.+
27 Mulungu ndi malo ako othawirapo kuyambira kalekale,+Iye wakunyamula mʼmanja ake omwe adzakhalapo mpaka kalekale.+ Adzathamangitsa mdani pamaso pako,+Ndipo adzanena kuti, ‘Awonongeni!’+