Yesaya 30:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Anthu akadzayamba kukhala ku Ziyoni, ku Yerusalemu,+ inu simudzaliranso.+ Mulungu adzakukomerani mtima akadzamva kulira kwanu kopempha thandizo. Akadzangomva kulira kwanu, nthawi yomweyo adzakuyankhani.+ Yesaya 55:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Inu nonse amene mukumva ludzu,+ bwerani mudzamwe madzi.+ Inu amene mulibe ndalama, bwerani mudzagule kuti mudye. Inde bwerani mudzagule vinyo ndi mkaka+ popanda ndalama ndiponso popanda mtengo.+
19 Anthu akadzayamba kukhala ku Ziyoni, ku Yerusalemu,+ inu simudzaliranso.+ Mulungu adzakukomerani mtima akadzamva kulira kwanu kopempha thandizo. Akadzangomva kulira kwanu, nthawi yomweyo adzakuyankhani.+
55 Inu nonse amene mukumva ludzu,+ bwerani mudzamwe madzi.+ Inu amene mulibe ndalama, bwerani mudzagule kuti mudye. Inde bwerani mudzagule vinyo ndi mkaka+ popanda ndalama ndiponso popanda mtengo.+