Yoweli 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nthawi imeneyo mʼmapiri akuluakulu mudzatuluka vinyo wotsekemera.+Mʼmapiri angʼonoangʼono mudzayenda mkaka.Ndipo mʼmitsinje yonse ya Yuda mudzayenda madzi. Kasupe adzatuluka mʼnyumba ya Yehova,+Ndipo adzathirira chigwa cha Mitengo ya Mthethe.
18 Nthawi imeneyo mʼmapiri akuluakulu mudzatuluka vinyo wotsekemera.+Mʼmapiri angʼonoangʼono mudzayenda mkaka.Ndipo mʼmitsinje yonse ya Yuda mudzayenda madzi. Kasupe adzatuluka mʼnyumba ya Yehova,+Ndipo adzathirira chigwa cha Mitengo ya Mthethe.