Salimo 89:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chifukwa chishango chathu ndi chochokera kwa Yehova,Ndipo mfumu yathu ndi yochokera kwa Woyera wa Isiraeli.+
18 Chifukwa chishango chathu ndi chochokera kwa Yehova,Ndipo mfumu yathu ndi yochokera kwa Woyera wa Isiraeli.+