Yesaya 49:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Fuulani mosangalala kumwamba inu ndipo sangalala iwe dziko lapansi.+ Mapiri asangalale ndipo afuule mosangalala.+ Chifukwa Yehova watonthoza anthu ake+Ndipo wachitira chifundo anthu ake ovutika.+ Yesaya 55:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa mudzapita mukusangalala,+Ndipo adzakubweretsani kwanu mwamtendere.+ Mukadzafika, mapiri ndi zitunda zidzafuula mosangalala,+Ndipo mitengo yonse yakutchire idzawomba mʼmanja.+
13 Fuulani mosangalala kumwamba inu ndipo sangalala iwe dziko lapansi.+ Mapiri asangalale ndipo afuule mosangalala.+ Chifukwa Yehova watonthoza anthu ake+Ndipo wachitira chifundo anthu ake ovutika.+
12 Chifukwa mudzapita mukusangalala,+Ndipo adzakubweretsani kwanu mwamtendere.+ Mukadzafika, mapiri ndi zitunda zidzafuula mosangalala,+Ndipo mitengo yonse yakutchire idzawomba mʼmanja.+