Deuteronomo 4:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Inuyo mwasonyezedwa zinthu zimenezi kuti mudziwe kuti Yehova ndi Mulungu woona.+ Palibenso Mulungu wina kupatulapo iyeyo.+ Deuteronomo 4:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Choncho mudziwe lero, ndipo muzikumbukira mumtima mwanu kuti Yehova ndi Mulungu woona, kumwamba ndiponso padziko lapansi.+ Palibenso wina.+ Deuteronomo 32:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Onani tsopano kuti ndine Mulungu,+Ndipo palibe Mulungu wina koma ine ndekha.+ Ndimapha komanso ndimapereka moyo.+ Ndimavulaza,+ ndipo ndidzachiritsa,+Palibe aliyense amene angapulumutse munthu mʼdzanja langa.+
35 Inuyo mwasonyezedwa zinthu zimenezi kuti mudziwe kuti Yehova ndi Mulungu woona.+ Palibenso Mulungu wina kupatulapo iyeyo.+
39 Choncho mudziwe lero, ndipo muzikumbukira mumtima mwanu kuti Yehova ndi Mulungu woona, kumwamba ndiponso padziko lapansi.+ Palibenso wina.+
39 Onani tsopano kuti ndine Mulungu,+Ndipo palibe Mulungu wina koma ine ndekha.+ Ndimapha komanso ndimapereka moyo.+ Ndimavulaza,+ ndipo ndidzachiritsa,+Palibe aliyense amene angapulumutse munthu mʼdzanja langa.+