Yesaya 43:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wako,Woyera wa Isiraeli, Mpulumutsi wako. Ndapereka Iguputo kuti akhale dipo* lako.Ndaperekanso Itiyopiya ndi Seba mʼmalo mwa iwe.
3 Chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wako,Woyera wa Isiraeli, Mpulumutsi wako. Ndapereka Iguputo kuti akhale dipo* lako.Ndaperekanso Itiyopiya ndi Seba mʼmalo mwa iwe.