23 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Mʼmasiku amenewo, amuna 10 ochokera mʼzilankhulo zonse za anthu a mitundu ina+ adzagwira mkanjo wa Myuda nʼkunena kuti: “Anthu inu tikufuna tipite nanu limodzi,+ chifukwa tamva kuti Mulungu ali ndi inu.”’”+