Deuteronomo 5:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Zikanakhala bwino kwambiri akanakhala ndi mtima wondiopa+ ndi kusunga malamulo anga+ nthawi zonse. Akanachita zimenezi zinthu zikanawayendera bwino, iwowo ndi ana awo mpaka kalekale!+ Salimo 81:13, 14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zikanakhala bwino ngati anthu anga akanandimvera,+Zikanakhala bwino ngati Isiraeli akanayenda mʼnjira zanga.+ 14 Ndikanagonjetsa adani awo mofulumira,Ndikanalanga adani awo ndi dzanja langa.+
29 Zikanakhala bwino kwambiri akanakhala ndi mtima wondiopa+ ndi kusunga malamulo anga+ nthawi zonse. Akanachita zimenezi zinthu zikanawayendera bwino, iwowo ndi ana awo mpaka kalekale!+
13 Zikanakhala bwino ngati anthu anga akanandimvera,+Zikanakhala bwino ngati Isiraeli akanayenda mʼnjira zanga.+ 14 Ndikanagonjetsa adani awo mofulumira,Ndikanalanga adani awo ndi dzanja langa.+