Yeremiya 50:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Thawani mʼBabulo,Tulukani mʼdziko la Akasidi,+Ndipo mukhale ngati mbuzi kapena nkhosa zamphongo zimene zikutsogolera gulu lonse. Chivumbulutso 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndinamva mawu ena kuchokera kumwamba akuti: “Tulukani mwa iye anthu anga,+ ngati simukufuna kugawana naye machimo ake ndiponso ngati simukufuna kulandira nawo ina ya miliri yake.+
8 “Thawani mʼBabulo,Tulukani mʼdziko la Akasidi,+Ndipo mukhale ngati mbuzi kapena nkhosa zamphongo zimene zikutsogolera gulu lonse.
4 Ndinamva mawu ena kuchokera kumwamba akuti: “Tulukani mwa iye anthu anga,+ ngati simukufuna kugawana naye machimo ake ndiponso ngati simukufuna kulandira nawo ina ya miliri yake.+