Yesaya 54:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa mudzafalikira mbali yakumanja ndi kumanzere. Ana ako adzatenga mitundu ya anthu kukhala yawo,Ndipo adzakhala mʼmizinda imene inasiyidwa yabwinja.+
3 Chifukwa mudzafalikira mbali yakumanja ndi kumanzere. Ana ako adzatenga mitundu ya anthu kukhala yawo,Ndipo adzakhala mʼmizinda imene inasiyidwa yabwinja.+