Yesaya 54:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Kwa ine, zimenezi zili ngati masiku a Nowa.+ Monga mmene ndinalumbirira kuti madzi amʼnthawi ya Nowa sadzamizanso dziko lapansi,+Ndikulumbiranso kuti sindidzakukwiyira kapena kukudzudzula.+ Yesaya 62:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova walumbira atakweza dzanja lake lamanja ndiponso mkono wake wamphamvu kuti: “Sindidzaperekanso mbewu zanu kwa adani anu kuti chikhale chakudya chawo,Ndipo alendo sadzamwa vinyo wanu watsopano amene munamupeza movutikira.+
9 “Kwa ine, zimenezi zili ngati masiku a Nowa.+ Monga mmene ndinalumbirira kuti madzi amʼnthawi ya Nowa sadzamizanso dziko lapansi,+Ndikulumbiranso kuti sindidzakukwiyira kapena kukudzudzula.+
8 Yehova walumbira atakweza dzanja lake lamanja ndiponso mkono wake wamphamvu kuti: “Sindidzaperekanso mbewu zanu kwa adani anu kuti chikhale chakudya chawo,Ndipo alendo sadzamwa vinyo wanu watsopano amene munamupeza movutikira.+