Salimo 137:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa kumeneko, anthu amene anatigwira ukapolo anatiuza kuti tiwaimbire nyimbo,+Amene ankatinyozawo ankafuna kuti tiwasangalatse. Iwo anati: “Tiimbireni nyimbo imodzi ya ku Ziyoni.” Yeremiya 50:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu a ku Isiraeli ali ngati nkhosa zomwazikana.+ Mikango ndi imene yawabalalitsa.+ Poyamba, mfumu ya Asuri inawadya.+ Kenako Mfumu Nebukadinezara* ya ku Babulo inakukuta mafupa awo.+
3 Chifukwa kumeneko, anthu amene anatigwira ukapolo anatiuza kuti tiwaimbire nyimbo,+Amene ankatinyozawo ankafuna kuti tiwasangalatse. Iwo anati: “Tiimbireni nyimbo imodzi ya ku Ziyoni.”
17 Anthu a ku Isiraeli ali ngati nkhosa zomwazikana.+ Mikango ndi imene yawabalalitsa.+ Poyamba, mfumu ya Asuri inawadya.+ Kenako Mfumu Nebukadinezara* ya ku Babulo inakukuta mafupa awo.+