7 Inu Mulungu, chikondi chanu chokhulupirika ndi chamtengo wapatali!+
Ana a anthu amabisala mumthunzi wa mapiko anu.+
8 Amamwa zakumwa zabwino zamʼnyumba yanu nʼkukhuta.+
Ndipo mumawachititsa kuti amwe zinthu zanu zosangalatsa zimene zimayenda ngati mtsinje.+