Yesaya 41:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mʼchipululu ndidzadzalamo mtengo wa mkungudza,Mtengo wa mthethe, mtengo wa mchisu ndi mtengo wa paini.+ Mʼchigwa chamʼchipululu ndidzadzalamo mtengo wa junipa,*Limodzi ndi mtengo wa ashi* komanso mtengo wofanana ndi mkungudza,+ Yesaya 60:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ulemerero wa Lebanoni udzabwera kwa iwe.+Mtengo wa junipa,* mtengo wa ashi* ndiponso mtengo wa mkungudza zidzabwera pa nthawi imodzi,+Kuti zikongoletse malo anga opatulika,Ndipo ine ndidzalemekeza malo oikapo mapazi anga.+
19 Mʼchipululu ndidzadzalamo mtengo wa mkungudza,Mtengo wa mthethe, mtengo wa mchisu ndi mtengo wa paini.+ Mʼchigwa chamʼchipululu ndidzadzalamo mtengo wa junipa,*Limodzi ndi mtengo wa ashi* komanso mtengo wofanana ndi mkungudza,+ Yesaya 60:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ulemerero wa Lebanoni udzabwera kwa iwe.+Mtengo wa junipa,* mtengo wa ashi* ndiponso mtengo wa mkungudza zidzabwera pa nthawi imodzi,+Kuti zikongoletse malo anga opatulika,Ndipo ine ndidzalemekeza malo oikapo mapazi anga.+
13 Ulemerero wa Lebanoni udzabwera kwa iwe.+Mtengo wa junipa,* mtengo wa ashi* ndiponso mtengo wa mkungudza zidzabwera pa nthawi imodzi,+Kuti zikongoletse malo anga opatulika,Ndipo ine ndidzalemekeza malo oikapo mapazi anga.+