Ekisodo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndi mulungu uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+ Mumasonyeza kuti ndinu woyera koposa,+ ndani angafanane ndi inu? Ndinu woyenera kuopedwa ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda. Inu mumachita zodabwitsa.+ Luka 1:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndiyeno Mariya ananena kuti: “Moyo wanga ukulemekeza Yehova,*+ Luka 1:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Chifukwa Wamphamvuyo wandichitira zazikulu ndipo dzina lake ndi loyera.+
11 Ndi mulungu uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+ Mumasonyeza kuti ndinu woyera koposa,+ ndani angafanane ndi inu? Ndinu woyenera kuopedwa ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda. Inu mumachita zodabwitsa.+