-
Yesaya 8:6, 7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 “Popeza anthu awa akana madzi a ku Silowa*+ amene amayenda pangʼonopangʼono,
Ndipo akusangalala ndi Rezini ndiponso mwana wa Remaliya,+
7 Yehova adzawabweretsera
madzi ambiri komanso amphamvu a mu Mtsinje*
Omwe ndi mfumu ya Asuri+ ndi ulemerero wake wonse.
Mfumuyo idzadzaza timitsinje take tonse
Nʼkusefukira mʼmphepete mwake monse
-