Salimo 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yehova ndi kuwala kwanga+ komanso ndi amene amandipulumutsa. Ndingaope ndani?+ Yehova ali ngati malo amene amateteza moyo wanga.+ Ndingachite mantha ndi ndani? Salimo 84:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa Yehova Mulungu ndi dzuwa+ ndiponso chishango.+Iye amatikomera mtima nʼkutipatsa ulemerero. Yehova sadzalephera kupereka chinthu chilichonse chabwinoKwa anthu amene amachita zinthu mokhulupirika.+
27 Yehova ndi kuwala kwanga+ komanso ndi amene amandipulumutsa. Ndingaope ndani?+ Yehova ali ngati malo amene amateteza moyo wanga.+ Ndingachite mantha ndi ndani?
11 Chifukwa Yehova Mulungu ndi dzuwa+ ndiponso chishango.+Iye amatikomera mtima nʼkutipatsa ulemerero. Yehova sadzalephera kupereka chinthu chilichonse chabwinoKwa anthu amene amachita zinthu mokhulupirika.+