Zefaniya 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Funafunani Yehova,+ inu nonse ofatsa* apadziko lapansi,Amene mumatsatira malamulo ake olungama.* Yesetsani kukhala olungama, yesetsani kukhala ofatsa.* Mwina mungadzabisike pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+ Machitidwe 10:34, 35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Petulo atamva zimenezi, anayamba kulankhula kuti: “Ndazindikira ndithu kuti Mulungu alibe tsankho.+ 35 Iye amalandira munthu wochokera mu mtundu uliwonse, amene amamuopa ndi kuchita chilungamo.+
3 Funafunani Yehova,+ inu nonse ofatsa* apadziko lapansi,Amene mumatsatira malamulo ake olungama.* Yesetsani kukhala olungama, yesetsani kukhala ofatsa.* Mwina mungadzabisike pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+
34 Petulo atamva zimenezi, anayamba kulankhula kuti: “Ndazindikira ndithu kuti Mulungu alibe tsankho.+ 35 Iye amalandira munthu wochokera mu mtundu uliwonse, amene amamuopa ndi kuchita chilungamo.+