Yesaya 28:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsopano pewani kunyoza+Kuti zingwe zanu asapitirize kuzimanga kwambiri,Chifukwa ndamva kuchokera kwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Ambuye Wamkulu Koposa,Kuti waganiza zoti awononge dziko lonseli.*+
22 Tsopano pewani kunyoza+Kuti zingwe zanu asapitirize kuzimanga kwambiri,Chifukwa ndamva kuchokera kwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Ambuye Wamkulu Koposa,Kuti waganiza zoti awononge dziko lonseli.*+