-
Mateyu 1:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Jese anabereka Mfumu Davide.+
Davide anabereka Solomo,+ yemwe mayi ake anali mkazi wa Uriya.
-
Luka 3:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Pamene Yesu+ anayamba ntchito yake anali ndi zaka pafupifupi 30.+ Anthu ankadziwa kuti Yesu anali mwana
wa Yosefe,+
mwana wa Heli,
-
Luka 3:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
mwana wa Obedi,+
mwana wa Boazi,+
mwana wa Salimoni,+
mwana wa Naasoni,+
-
Machitidwe 13:22, 23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Atamuchotsa ameneyu, anawapatsa Davide kuti akhale mfumu yawo.+ Iyeyu Mulungu anamuchitira umboni kuti, ‘Ndapeza Davide mwana wa Jese,+ munthu wapamtima panga.+ Ameneyu adzachita zonse zimene ndikufuna.’ 23 Mogwirizana ndi lonjezo lake, kuchokera pa mbadwa* za munthu ameneyu, Mulungu wabweretsa mpulumutsi mu Isiraeli, amene ndi Yesu.+
-
-
-
-
-
-
-