Genesis 49:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndodo yachifumu sidzachoka kwa Yuda,+ ndiponso chibonga cha wolamulira sichidzachoka pakati pa mapazi ake, mpaka Silo* atabwera.+ Ndipo mitundu ya anthu idzamumvera.+ Yesaya 49:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Taona! Ineyo ndidzakwezera dzanja langa mitundu ya anthu,Ndipo anthu a mitundu ina ndidzawakwezera chizindikiro.+ Iwo adzakubweretsera ana ako aamuna atawanyamula mʼmanja,*Ndipo ana ako aakazi adzawanyamula paphewa.+ Yesaya 62:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Dutsani mʼmageti, dutsani mʼmageti. Lambulani njira kuti anthu adutse.+ Konzani msewu, konzani msewu waukulu. Muchotsemo miyala.+ Anthu a mitundu yosiyanasiyana muwakwezere chizindikiro+
10 Ndodo yachifumu sidzachoka kwa Yuda,+ ndiponso chibonga cha wolamulira sichidzachoka pakati pa mapazi ake, mpaka Silo* atabwera.+ Ndipo mitundu ya anthu idzamumvera.+
22 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Taona! Ineyo ndidzakwezera dzanja langa mitundu ya anthu,Ndipo anthu a mitundu ina ndidzawakwezera chizindikiro.+ Iwo adzakubweretsera ana ako aamuna atawanyamula mʼmanja,*Ndipo ana ako aakazi adzawanyamula paphewa.+
10 Dutsani mʼmageti, dutsani mʼmageti. Lambulani njira kuti anthu adutse.+ Konzani msewu, konzani msewu waukulu. Muchotsemo miyala.+ Anthu a mitundu yosiyanasiyana muwakwezere chizindikiro+