4 Munthu amene iwo amati ndi wabwino kwambiri, ali ngati minga,
Ndipo munthu amene amati ndi wachilungamo kwambiri, ndi woipa kuposa mpanda wa mitengo yaminga.
Tsiku limene alonda awo ananena komanso limene adzaweruzidwe lidzafika ndithu.+
Pa tsikulo iwo adzathedwa nzeru.+