-
Yoweli 2:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
‘Inu Yehova, mverani chisoni anthu anu,
Ndipo musachititse manyazi cholowa chanu,
Kuti anthu a mitundu ina awalamulire.
Anthu a mitundu ina asanene kuti: “Kodi Mulungu wawo ali kuti?”’+
-