Yesaya 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Sizidzavulazana+Kapena kuwonongana mʼphiri langa lonse loyera,+Chifukwa dziko lapansi lidzadzaza ndi anthu odziwa YehovaNgati mmene madzi amadzazira mʼnyanja.+ Yesaya 65:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mmbulu ndi mwana wa nkhosa zidzadyera pamodzi,Mkango udzadya udzu ngati ngʼombe yamphongo,+Ndipo chakudya cha njoka chidzakhala fumbi. Zimenezi sizidzapweteka aliyense kapena kuwononga chilichonse mʼphiri langa lonse loyera,”+ akutero Yehova.
9 Sizidzavulazana+Kapena kuwonongana mʼphiri langa lonse loyera,+Chifukwa dziko lapansi lidzadzaza ndi anthu odziwa YehovaNgati mmene madzi amadzazira mʼnyanja.+
25 Mmbulu ndi mwana wa nkhosa zidzadyera pamodzi,Mkango udzadya udzu ngati ngʼombe yamphongo,+Ndipo chakudya cha njoka chidzakhala fumbi. Zimenezi sizidzapweteka aliyense kapena kuwononga chilichonse mʼphiri langa lonse loyera,”+ akutero Yehova.