Yesaya 57:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Ndikulenga chipatso cha milomo. Mtendere wosatha udzaperekedwa kwa amene ali kutaliNdiponso kwa amene ali pafupi+ ndipo ndidzamʼchiritsa,” akutero Yehova. Yeremiya 33:6, 7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ‘Ine ndichiritsa anthu amumzindawu nʼkuwapatsa thanzi labwino.+ Ndiwachiritsa nʼkuwapatsa mtendere wambiri ndi choonadi chochuluka.+ 7 Anthu a mu Yuda ndi a mu Isiraeli amene anatengedwa kupita kudziko lina ndidzawabwezeretsa+ ndipo adzakhalanso ngati mmene analili poyamba.+
19 “Ndikulenga chipatso cha milomo. Mtendere wosatha udzaperekedwa kwa amene ali kutaliNdiponso kwa amene ali pafupi+ ndipo ndidzamʼchiritsa,” akutero Yehova.
6 ‘Ine ndichiritsa anthu amumzindawu nʼkuwapatsa thanzi labwino.+ Ndiwachiritsa nʼkuwapatsa mtendere wambiri ndi choonadi chochuluka.+ 7 Anthu a mu Yuda ndi a mu Isiraeli amene anatengedwa kupita kudziko lina ndidzawabwezeretsa+ ndipo adzakhalanso ngati mmene analili poyamba.+