Yesaya 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova akadzatsuka nyansi* za ana aakazi a Ziyoni+ ndiponso akadzatsuka magazi amene Yerusalemu anakhetsa, pogwiritsa ntchito mzimu wa chiweruzo komanso mzimu woyaka moto,+ Yesaya 48:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Taonani! Ndinakuyengani koma osati ngati mmene amayengera siliva.+ Ndinakuyesani* mʼngʼanjo ya mavuto.+
4 Yehova akadzatsuka nyansi* za ana aakazi a Ziyoni+ ndiponso akadzatsuka magazi amene Yerusalemu anakhetsa, pogwiritsa ntchito mzimu wa chiweruzo komanso mzimu woyaka moto,+
10 Taonani! Ndinakuyengani koma osati ngati mmene amayengera siliva.+ Ndinakuyesani* mʼngʼanjo ya mavuto.+