Numeri 34:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Upereke malangizo awa kwa Aisiraeli: ‘Awa ndi malire a dziko la Kanani, dziko limene ndidzakupatseni kuti likhale cholowa chanu.+ Numeri 34:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno kuchokera ku Azimoni, malirewo akalowere kuchigwa cha Iguputo* mpaka kukathera ku Nyanja Yaikulu.*+
2 “Upereke malangizo awa kwa Aisiraeli: ‘Awa ndi malire a dziko la Kanani, dziko limene ndidzakupatseni kuti likhale cholowa chanu.+
5 Ndiyeno kuchokera ku Azimoni, malirewo akalowere kuchigwa cha Iguputo* mpaka kukathera ku Nyanja Yaikulu.*+