Yesaya 51:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zinthu ziwiri izi zakugwera. Ndi ndani amene akumvere chisoni? Kuwonongedwa ndi kusakazidwa, njala ndi lupanga!+ Kodi ndi ndani amene akutonthoze?+ Maliro 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Misewu yopita ku Ziyoni ikulira chifukwa palibe amene akupita kuchikondwerero.+ Mageti ake onse awonongedwa.+ Ansembe ake akuusa moyo. Anamwali* ake agwidwa ndi chisoni ndipo iyeyo akumva ululu mumtima.
19 Zinthu ziwiri izi zakugwera. Ndi ndani amene akumvere chisoni? Kuwonongedwa ndi kusakazidwa, njala ndi lupanga!+ Kodi ndi ndani amene akutonthoze?+
4 Misewu yopita ku Ziyoni ikulira chifukwa palibe amene akupita kuchikondwerero.+ Mageti ake onse awonongedwa.+ Ansembe ake akuusa moyo. Anamwali* ake agwidwa ndi chisoni ndipo iyeyo akumva ululu mumtima.