Yesaya 41:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Udzapeta mapiri ndi zitundazoNdipo mphepo idzaziuluza.Mphepo yamkuntho idzazimwaza. Iweyo udzasangalala chifukwa cha Yehova,+Ndipo udzadzitama chifukwa cha Woyera wa Isiraeli.”+
16 Udzapeta mapiri ndi zitundazoNdipo mphepo idzaziuluza.Mphepo yamkuntho idzazimwaza. Iweyo udzasangalala chifukwa cha Yehova,+Ndipo udzadzitama chifukwa cha Woyera wa Isiraeli.”+