Mika 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Tsoka kwa anthu amene amakonza chiwembu,Amene akagona pabedi pawo, amaganizira kuti achite zoipa. Ndipo mʼmawa kukacha, amazichitadi.Chifukwa ali ndi mphamvu zochitira zimenezo.+
2 “Tsoka kwa anthu amene amakonza chiwembu,Amene akagona pabedi pawo, amaganizira kuti achite zoipa. Ndipo mʼmawa kukacha, amazichitadi.Chifukwa ali ndi mphamvu zochitira zimenezo.+