Deuteronomo 32:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mkwiyo wanga wayatsa moto+Umene udzayaka mpaka kukafika pansi penipeni pa Manda,*+Ndipo udzapsereza dziko lapansi ndi zokolola zake,Komanso udzayatsa maziko a mapiri. Nahumu 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye atapsa mtima, ndani angaime pamaso pake?+ Iye atakwiya, ndani angalimbe mtima kuima pamaso pake?+ Mkwiyo wake adzaukhuthula ngati moto,Ndipo miyala idzaphwanyidwa chifukwa cha iye. Aheberi 12:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chifukwa Mulungu wathu ali ngati moto wowononga.+
22 Mkwiyo wanga wayatsa moto+Umene udzayaka mpaka kukafika pansi penipeni pa Manda,*+Ndipo udzapsereza dziko lapansi ndi zokolola zake,Komanso udzayatsa maziko a mapiri.
6 Iye atapsa mtima, ndani angaime pamaso pake?+ Iye atakwiya, ndani angalimbe mtima kuima pamaso pake?+ Mkwiyo wake adzaukhuthula ngati moto,Ndipo miyala idzaphwanyidwa chifukwa cha iye.