1 Mafumu 19:5, 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako anagona pansi pa kamtengo kaja mpaka tulo tinamʼpeza. Mwadzidzidzi kunabwera mngelo ndipo anamukhudza+ nʼkumuuza kuti: “Dzuka udye.”+ 6 Atayangʼana, anaona kuti kumutu kwake kuli mkate wozungulira pamiyala yotentha komanso jagi* ya madzi. Eliya anadya nʼkumwa ndipo anagonanso. Salimo 34:9, 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Opani Yehova, inu oyera ake onse,Chifukwa onse amene amamuopa sasowa kanthu.+ כ [Kaph] 10 Ngakhale mikango yamphamvu* ingakhale ndi njala chifukwa chosowa chakudya.Koma anthu amene akufunafuna Yehova sadzasowa chilichonse chabwino.+ Yesaya 65:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Atumiki anga adzadya, koma inu mudzakhala ndi njala.+ Atumiki anga adzamwa,+ koma inu mudzakhala ndi ludzu. Atumiki anga adzasangalala,+ koma inu mudzachita manyazi.+
5 Kenako anagona pansi pa kamtengo kaja mpaka tulo tinamʼpeza. Mwadzidzidzi kunabwera mngelo ndipo anamukhudza+ nʼkumuuza kuti: “Dzuka udye.”+ 6 Atayangʼana, anaona kuti kumutu kwake kuli mkate wozungulira pamiyala yotentha komanso jagi* ya madzi. Eliya anadya nʼkumwa ndipo anagonanso.
9 Opani Yehova, inu oyera ake onse,Chifukwa onse amene amamuopa sasowa kanthu.+ כ [Kaph] 10 Ngakhale mikango yamphamvu* ingakhale ndi njala chifukwa chosowa chakudya.Koma anthu amene akufunafuna Yehova sadzasowa chilichonse chabwino.+
13 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Atumiki anga adzadya, koma inu mudzakhala ndi njala.+ Atumiki anga adzamwa,+ koma inu mudzakhala ndi ludzu. Atumiki anga adzasangalala,+ koma inu mudzachita manyazi.+