-
Ekisodo 18:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Pakati pa anthuwa, usankhepo amuna oyenerera,+ oopa Mulungu, okhulupirika, odana ndi kupeza phindu mwachinyengo.+ Amenewa uwaike kuti akhale atsogoleri a anthuwa, ndipo pakhale atsogoleri a magulu a anthu 1,000, atsogoleri a magulu a anthu 100, atsogoleri a magulu a anthu 50 ndi atsogoleri a magulu a anthu 10.+
-